Featured Posts

Chat Platform

Image
HealthChat Feed Create a Post Post

MBUTO YA KALULU INAKULA NTADZAONANI

MBUTO YA KALULU INAKULA NTADZAONANI

Pamene anthu ambiri amasinjirira mlandu kapena nkhani, anthu ena odziwa kuti zimenezo nzonama amanena mwambi umenewu, amati, 

"Kanthu kamakula ndikukalapa." Tanthauzo lache ndilo:

Munthu wina anapeza pomwe panagona kalulu nati,

"Tadzaonani pano panagona kalulu." 

Tsono anthu ambiri pofika nalapa, mau anawanda-wanda ndipo panakhala bande lalikulu monga ngati mbuto ya njobvu.

_____________________________________________________________

Contact us:


Mtonga Isaac Pharmacy,

Ng'ombe Township,

#16/24 Off Zambezi road,

Email: mtongaisaacpharmacy@gmail.com,

Tel: +260974272433/+260966399444,

Lusaka, Zambia.

_______________________________________
_______________________________________
________________________________________

Mtonga Isaac Pharmacy Zambia

NAME & SURNAME:
EMAIL ADDRESS
MESSAGE:
_______________________________________

Comments

Popular Posts

CERVICAL STENOSIS(BLOCKED CERVIX) AND TREATMENT

ERECTILE DYSFUNCTION (IMPOTENCE) AND TREATMENT

PELVIC INFLAMMATION DISEASE (PID) AND TREATMENT

AMENORRHEA AND TREATMENT

ENDOMETRIOSIS AND TREATMENT

MISCARRIAGE (PREGNANCY LOSE) AND TREATMENT

CD4 - CD8 COUNT AND TREATMENT