Featured Posts

Chat Platform

Image
HealthChat Feed Create a Post Post

CHETE-CHETE SAUTSA NYAMA


CHETE-CHETE SAUTSA NYAMA

Panchito ndi paulendo pafunika wina wodzutsa anthu amene amangokhala chete. 

Mwambi umenewu unenedwa pa mlandu poyamba kulonjera, ngati anthu angokhala chete osalonjera mlandu. 

Nthawi yina ngakhale pakati pa mlandu anthu atafunsa funso ndipo akamapanda kuyankha msanga, ena amauponya msanga, pompo pamaoneka ena onena nati, "Siuwo kumeneko yankhani."

*Kufanizira kwache kwa mwambi uwu afanizira uzimba wamaukonde. Posaka nyama osakawo samangosaka chete ai koma kukuwa, ngati angosaka kachetechete, nyama sizingabvumbuluke. 

Odikira okha amakhala chete. Odikira ndi chimodzi-modzi oweruza mlandu, osaka ndiwo amene anena mlandu pamodzi ndi maphungu. Choncho omvera angakhale chete, si ndiwo outsa nkhani, koma onenawo.

KONKHANI MIYAMBI YINA PASIPA

www.miyambi.com

_______________________________________________________________

Contact us:


Mtonga Isaac Pharmacy,

Ng'ombe Township,

#16/24 Off Zambezi road,

Email: mtongaisaacpharmacy@gmail.com,

Tel: +260974272433/+260966399444,

Lusaka, Zambia.

_______________________________________
_______________________________________
________________________________________

Mtonga Isaac Pharmacy Zambia

NAME & SURNAME:
EMAIL ADDRESS
MESSAGE:
_______________________________________

Comments

Popular Posts

CERVICAL STENOSIS(BLOCKED CERVIX) AND TREATMENT

ERECTILE DYSFUNCTION (IMPOTENCE) AND TREATMENT

PELVIC INFLAMMATION DISEASE (PID) AND TREATMENT

AMENORRHEA AND TREATMENT

ENDOMETRIOSIS AND TREATMENT

MISCARRIAGE (PREGNANCY LOSE) AND TREATMENT

CD4 - CD8 COUNT AND TREATMENT