Featured Posts

Download BlueEye Lite the Social Media designed for you

Image
DOWNLOAD BLUEEYE LITE — THE SOCIAL PLATFORM DESIGNED FOR YOU 🌍  BlueEye Lite  is not just another app—it’s a bold, inclusive social media platform built to empower creators, connect communities, and give every user a voice. Whether you're posting, reacting, or discovering new content,  BluEye Lite  is designed to feel natural, secure, and universally accessible. 🛠️  Crafted and branded by Dr. Mtonga N. Isaac , a visionary platform architect based in Lusaka, Zambia,  BlueEye Lite  reflects a deep commitment to privacy, clarity, and real-world usability. Every feature is built with purpose—from secure onboarding to expressive media sharing. ✨ What makes  BlueEye Lite  stand out: ✅  Clean, responsive design  for mobile friendly ✅  Secure login  with phone or email—your data stays yours ✅  Open posting  with reactions, replies, and media previews ✅  Modular features  that evolve with your needs 📢  Y...

NYANJA/CHEWA PROVERBS BY DR MTONGA N. ISAAC


NYANJA PROVERBS RE-EDITED BY DR MTONGA N. ISAAC

Kale-kale mitundu yonse ya anthu inali ndi zochita ndi zonena-nena za mitundu mitundu. Anali ndi zina zokambirana akulu okha-okha, zinanso zokambira ana
ao. Anali ndi nthanthi ndi miyambi ya mitundu-mitundu imene inali ndi ziphunzitso zosiyana-siyana.

Miyambi yina inali yonena pa mirandu mophiphiritsa koma yokhala ndi zolozera zache, kotero anthu nadziwa ponena. Yina inali yakuphunzitsa za chikhalidwe cha
anthu, za umphala, za pabanja, za nthenda, za imfa ndi zina zotero.

Zophunzira zambiri zinakolekedwa ku miyambi. Ngakhale sanadziwe kulemba ndi kuwerenga koma anangozikumbukira ponena-nena malinga ndi kanthu kache koonekera. Masiku ano miyambiyo imamveka kamodzi-kamodzi ikunenedwa ndi anthu. Ana ambiri a lero saidziwa chifukwa sinalembedwe.

Makolo athu anangopitiriza mwakungokamba mwa
mibadwo-mibadwo kufikira tsopano. Chifukwa cha chimenechi zambiri zangoferamo zosakumbukiridwa
chifukwa cha kubvuta kuzikumbukira m'mutu mokha.

Tayesa kusonkhanitsa miyambi imene iri yofunika ndi anthu ambiri kotero kuti ana a ana athu asadzaiwale nzeru zochitidwa kale ndi makolo ao koma apezemo maziko a nzeru zatsopano ndi zamtsogolo. Popanda
kudziwa miyambi yakale, tidzakhala anthu obvutika pophunzira zatsopano chifukwa chosowa popondera (maziko) polimba pamene makolo athu anatikonzera.

Miyambi yina yolembedwayi ingakhale yothangata oweruza a lero m'dziko lino pozenga mirandu yao, yina.

SANKHANI MWAMBI MUSIMU:
______________________________________________________________

Contact us:

Mtonga Isaac Pharmacy,
Ng'ombe Township,
#16/24 Off Zambezi road,
Email: mtongaisaacpharmacy@gmail.com,
Tel: +260974272433/+260966399444,
Lusaka, Zambia.
_______________________________________
_______________________________________
________________________________________

Mtonga Isaac Pharmacy Zambia

NAME & SURNAME:
EMAIL ADDRESS
MESSAGE:
_______________________________________

Comments

Popular Posts

CERVICAL STENOSIS(BLOCKED CERVIX) AND TREATMENT

ERECTILE DYSFUNCTION (IMPOTENCE) AND TREATMENT

PELVIC INFLAMMATION DISEASE (PID) AND TREATMENT

MISCARRIAGE (PREGNANCY LOSE) AND TREATMENT

AMENORRHEA AND TREATMENT

TWIN PREGNANCY AND GUIDELINES

ENDOMETRIOSIS AND TREATMENT