Featured Posts

Chat Platform

Image
HealthChat Feed Create a Post Post

KULAMULA BVUMBWE NKULINGA ULI NDI NKHUKU

KULAMULA BVUMBWE NKULINGA ULI NDI NKHUKU

Mwambi wonena anthu opalamula mlandu, ndiko kuti akapalamula, adzikhala ndi podzikhulupirira. 

Nthano yache ya mwambiwu ndiyo: 

Munthu ndi bvumbwe anachitana mlandu, ndipo mlandu unabwerera munthu.

Anthu polamula mlandu anati, "Mlipiretu mnzako wamuchimwira." 

Munthuyo popeza analibe nkhuku anangotenga chimanga nampatsa, koma bvumbwe anakana nati, "Ine chimanga, mapira ndi zonse zina sindimadya koma nkhuku basi." 

Potero pakusowa cholipira, mlandu unakula.

KONKHANI MIYAMBI YINA PASIPA

www.miyambi.com

_______________________________________________________________

Contact us:


Mtonga Isaac Pharmacy,

Ng'ombe Township,

#16/24 Off Zambezi road,

Email: mtongaisaacpharmacy@gmail.com,

Tel: +260974272433/+260966399444,

Lusaka, Zambia.

_______________________________________
_______________________________________
________________________________________

Mtonga Isaac Pharmacy Zambia

NAME & SURNAME:
EMAIL ADDRESS
MESSAGE:
_______________________________________

Comments

Popular Posts

CERVICAL STENOSIS(BLOCKED CERVIX) AND TREATMENT

ERECTILE DYSFUNCTION (IMPOTENCE) AND TREATMENT

PELVIC INFLAMMATION DISEASE (PID) AND TREATMENT

AMENORRHEA AND TREATMENT

ENDOMETRIOSIS AND TREATMENT

MISCARRIAGE (PREGNANCY LOSE) AND TREATMENT

CD4 - CD8 COUNT AND TREATMENT