Featured Posts
MUBVI WOYANG'ANIRA SUCHEDWA KUGWERA M'MASO
- Get link
- X
- Other Apps
MUBVI WOYANG'ANIRA SUCHEDWA KUGWERA
M'MASO
Mwambi wonenedwa poweruza mlandu wa munthu amene wakwatira pamudzi ndipo akulu amuweruza kuti, "Kachoke pamudzipo chifukwa cha zobvuta zoonekera."
Mwini wokwatirayo akamaumirira kuti, "Ndapakonda pamudzipo," akulu amati,
'Nchimodzi-modzi mubvi umene anzako alikukuloza kuti akulase, ndipo iwe ungoima wosathawa. Posachedwa ulasa m'maso.
'Chinthu chobvuta ukachiyang'anira kufikira chitakula, mtsogolo usauka nacho.
Mau akuti: "Ndapakonda," ali ndi mwambi wache.
Ngati wina ati, "Ndapakonda pa mudzi pano," akulu amati:
KONKHANI MIYAMBI YINA PASIPA
____________________________________________________________
Contact us:
Mtonga Isaac Pharmacy,
Ng'ombe Township,
#16/24 Off Zambezi road,
Email: mtongaisaacpharmacy@gmail.com,
Tel: +260974272433/+260966399444,
Lusaka, Zambia.
_______________________________________ _______________________________________
Comments
Post a Comment