Featured Posts

Chat Platform

Image
HealthChat Feed Create a Post Post

TSOKA MSINDE CHIMANGA CHIRINDA MOTO

TSOKA MSINDE CHIMANGA CHIRINDA MOTO

Pamene anthu ayesedwa olakwa iwo eni alikudziwa kuti sitinachimwatu ife koma eni ache, alipo anganene mwambi umenewu. 

Iri ndi tsoka la msinde. 

Tanthauzo lache ndi kuti munthu popita kumunda amanka ndi ganizo lakuti ndikafune chimanga chachiwisi ndioche, ndidye. 

Popita athyola chimanga pamodzi ndi msinde wache, koma popeza chimanga chimafunika kuchikolezera moto, pamapita nthawi, ndipo amayamba kudya msinde, chimanga namadya potsirizira.

KONKHANI MIYAMBI YINA PASIPA

www.miyambi.com

____________________________________________________________

Contact us:


Mtonga Isaac Pharmacy,

Ng'ombe Township,

#16/24 Off Zambezi road,

Email: mtongaisaacpharmacy@gmail.com,

Tel: +260974272433/+260966399444,

Lusaka, Zambia.

_______________________________________
_______________________________________
________________________________________

Mtonga Isaac Pharmacy Zambia

NAME & SURNAME:
EMAIL ADDRESS
MESSAGE:
_______________________________________

Comments

Popular Posts

CERVICAL STENOSIS(BLOCKED CERVIX) AND TREATMENT

ERECTILE DYSFUNCTION (IMPOTENCE) AND TREATMENT

PELVIC INFLAMMATION DISEASE (PID) AND TREATMENT

AMENORRHEA AND TREATMENT

ENDOMETRIOSIS AND TREATMENT

MISCARRIAGE (PREGNANCY LOSE) AND TREATMENT

CD4 - CD8 COUNT AND TREATMENT