Featured Posts

Chat Platform

Image
HealthChat Feed Create a Post Post

TSIKU LIMODZI SIRIOZA MBEWA


TSIKU LIMODZI SIRIOZA MBEWA

Mwambi uwu umanenedwa pakugoneka mlandu, ena nakana kuti, "Iai, tifuna utheretu lero lomwe." 

Akulu amafanizira ndi munthu wopha mbewa kuti akapanda kuphika lero ndi kusiya mpaka mmawa sizingabvunde, ngakhale ziri zobvunda msanga-msanga. 

Nchimodzi-modzi ndi mlandu kuusunga tsiku limodzi lokha sungabvunde. 

Kutsatira mau awo achulidwawo lero lomwe, pali mwambi wakuti:

Lero lomwe linadetsa mnthengu

KONKHANI MIYAMBI YINA PASIPA

www.miyambi.com

______________________________________________________________

Contact us:


Mtonga Isaac Pharmacy,

Ng'ombe Township,

#16/24 Off Zambezi road,

Email: mtongaisaacpharmacy@gmail.com,

Tel: +260974272433/+260966399444,

Lusaka, Zambia .

_______________________________________
_______________________________________
________________________________________

Mtonga Isaac Pharmacy Zambia

NAME & SURNAME:
EMAIL ADDRESS
MESSAGE:
_______________________________________

Comments

Popular Posts

CERVICAL STENOSIS(BLOCKED CERVIX) AND TREATMENT

ERECTILE DYSFUNCTION (IMPOTENCE) AND TREATMENT

PELVIC INFLAMMATION DISEASE (PID) AND TREATMENT

AMENORRHEA AND TREATMENT

ENDOMETRIOSIS AND TREATMENT

MISCARRIAGE (PREGNANCY LOSE) AND TREATMENT

CD4 - CD8 COUNT AND TREATMENT